Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Anthu Okwatirana Komanso Mabanja

Baibulo lomwe ndi buku la anthu onse limapereka malangizo omwe angathandize kuti banja lanu likhale losangalala komanso kuti mulere bwino ana anu. a

a Mu chigawo chino, tasintha maina a anthu ena omwe tawagwira mawu.

ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA

Muziphunzitsa Mwana Wanu Kukhala Wopirira

Mukaona kuti mwana wanu akuvutika kugwira ntchito inayake, kodi muyenera kungothamangira kumuthandiza? Kapena mungamuphunzitse kuthana ndi mavuto?

Kulera Ana

Laibulale

Banja Lanu Likhoza Kukhala Losangalala

Mukhoza kukhala ndi banja losangalala mukamatsatira mfundo za m’Baibulo.