Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Chikondi Chimagonjetsa Kupanda Chilungamo

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Chikondi Chimagonjetsa Kupanda Chilungamo

Alwande ndi Emma akufotokoza mmene malonjezo a m’Baibulo anawathandizira kugwiritsa ntchito mtima wawo wofuna kuthandiza anthu, powafotokozera kuti mavuto onse adzatheratu. Pa nthawi imodzimodziyo akusangalala kukhala mogwirizana ndi anthu ena.