Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GALAMUKANI! Na. 3 2018 | Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa

Kodi tingapeze kuti mfundo zomwe zingatithandize tikaferedwa?

Nkhani za m’magaziniyi zikufotokoza zimene zimachitika munthu amene timamukonda akamwalira. Zikufotokozanso zimene mungachite kuti muthe kupirira mukaferedwa.

 

Kuvutika Maganizo Chifukwa Choferedwa

Kumwalira kwa mwamuna kapena mkazi wako, wachibale kapena mnzako, kumasokoneza maganizo kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mumve zomwe akatswiri komanso anthu ena omwe anaferedwa ananena.

Mavuto Amene Mungakumane Nawo

Kodi munthu amene waferedwa angakumane ndi mavuto otani?

Zimene Zingakuthandizeni Mukaferedwa​—Zimene Mungachite Panopa

Anthu amene okondedwa awo anamwalira anaona kuti pali njira zingapo zomwe zinawathandiza kuti azisangalala.

Mfundo Zofunika Kwambiri Kwa Anthu Omwe Aferedwa

Baibulo limapereka malangizo othandiza kwambiri kwa anthu omwe aferedwa.

Magaziniyi Ili ndi Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa

Magaziniyi ili ndi mfundo zothandiza komanso kulimbikitsa anthu amene anaferedwa.