Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.

Uganda

808 Lubowa Estate Road

Lubowa

KAMPALA

UGANDA

+256 41-4-201-194

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 30

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 8 izi: Chiacholi, Chiateso, Chilukonzo, Chiluganda, Chilugibara, Chimadi, Chirunyankore ndiponso Chirutoro.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.