NSANJA YA MLONDA September 2015 | Mmene mungalimbanilane ndi nkhawa

Anthu mamiliyoni ambili amakumana ndi ngozi zacilengedwe, koma ena amalimbana ndi mavuto amenewa ali ndi nkhawa zocepa pamene ena amakhala ndi nkhawa zambili. Amacita bwanji zimenezo?

NKHANI YA PACIKUTO

Anthu Kulikonse Ali Ndi Nkhawa

Kafukufuku akuonetsa kuti ngakhale nkhawa yaing’ono ingacititse munthu kufa msanga. Kodi mungalimbane bwanji ndi nkhawa?

NKHANI YA PACIKUTO

Nkhawa Zokhudza Ndalama

Mwamuna wina anakwanitsa kusamalila banja lake ngakhale pamene zinthu zofunika paumoyo zinakwela mtengo kufika ku mabiliyoni.

NKHANI YA PACIKUTO

Nkhawa Zokhudza Banja

Nkhani ya mkazi wosiidwa ndi mwamuna wake, kutha kwa banja, ndi kupilila mavuto, ionetsa ubwino wokhala ndi cikhulupililo.

NKHANI YA PACIKUTO

Nkhawa Zokhudza Ngozi

Kodi mungalimbane bwanji ndi nkhondo, ciwawa, kuonongeka kwa cilengedwe, kusintha kwa nyengo, ndi milili?

BAIBO IMASINTHA ANTHU

Umoyo Wanga Unali Kuipilaipilabe

Stephen McDowell anali mnyamata waciwawa, koma kumangidwa kwa anzake amene anapha munthu, kunamucitsa kuyamba kuphunzila Baibulo.

TENGELANI CIKHULUPILILO CAWO

“Ine Ndinauka Monga Mai mu Isiraeli”

Kodi nkhani ya m’Baibulo ya Debora itiphunzitsa ciani za cikhulupililo ndi kulimba mtima?

Kuyankha Mafunso a m’Baibulo

Kodi colinga ca moyo n’ciani? N’cifukwa ciani Mulungu anapanga anthu?

Madanga Ena Opezeka pa Intaneti

Kodi Nkhondo ya Aramagedo N’ciyani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibo. Koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imachulidwa m’Baibo lonse.