Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Angola

Rua de Talatona N°1 (Próximo da Angola Telecom)

LUANDA SUL

ANGOLA

+244 222-460-192

+244 222-460-211

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Mphindi 45

Zimene Timacita

Timamasulila Mabaibulo ndi mabuku ofotokoza Baibulo m’Cicokwe, Cikikongo, Cikimbundu, Cingangela, Cinyaneka, Ciumbundu. Ndiponso timatumiza magazini pafupifupi 1 miliyoni pa caka kumipingo yoposa 1,000.

Tengani kapepala koonetsa malo.