Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Britain

Watch Tower

The Ridgeway

LONDON

NW7 1RN

ENGLAND

+44 20-8906-2211

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

9:45hrs ; 13:15hrs ; 15:00hrs

Nthawi yoona malo: Ola Limodzi ndi mphindi 30

Zimene Timacita

Timasindikiza magazini oposa 200 miliyoni ndi tumabuku caka ciliconse ndiponso kuwatumiza ku maiko 100. Timaonetsenso cithunzithunzi ca zinthu zakale cokhala ndi mau akuti: “Baibulo mu Britain.”

Tengani kapepala koonetsa malo.