Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Italy

Congregazione Cristiana Dei Testimoni di Geova

Via della Bufalotta 1281

I-00138 ROME RM

ITALY

+39 06-872941

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:00hrs mpaka 15:30hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Citaliyana ndi cinenelo ca manja ca ku Italy. Timapanganso ma CD a zofalitsa ndi mavidiyo. Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova za m’tumagulu ndi m’mipingo yoposa 3,000 ya m’dzikoli ndi m’maiko ena.

Tengani kapepala koonetsa malo.