Onani zimene zilipo

Zifukwa Zokhalila na Cikhulupililo—Niziyendela Mfundo za Mulungu Kapena Zanga

Zifukwa Zokhalila na Cikhulupililo—Niziyendela Mfundo za Mulungu Kapena Zanga

Hugo na Clara akuona mmene kutsatila mfundo za Yehova kunawathandizila kupewa kusonkhezeledwa na anzawo, pamene anali ku sukulu na kupewa zotulukapo zoipa zobwela kaamba kosatsatila malamulo a Mulungu.