Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Machitidwe a Atumwi

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Machitidwe a Atumwi

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’buku la Machitidwe, limene limafotokoza mmene mpingo wachikhristu unayambira komanso chimene chinachititsa kuti upitirizebe kukula ngakhale kuti panali mavuto ambiri.