Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Akorinto

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Akorinto

Werengani kalata yoyamba yopita kwa Akhristu a ku Korinto yomwe ili ndi malangizo ouziridwa pa nkhani yochita zinthu mogwirizana, kupewa chiwerewere komanso khalidwe lofunika kwambiri la chikondi.