Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Akorinto

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Akorinto

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’kalata yachiwiri yopita kwa Akhristu a ku Korinto. Kalatayi ili ndi malangizo ouziridwa okhudza chifundo cha Yehova komanso chilungamo chake.