Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Tito

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Tito

Onerani vidiyoyi kuti muone mmene tingapindulire tikamatsatira malangizo omwe mtumwi Paulo anapereka kwa Tito, yemwe anali ndi ntchito yaikulu yoti agwire pachilumba cha Kerete.