Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mfundo Zokhudza Buku la Esitere

Mfundo Zokhudza Buku la Esitere

Mfundo zokuthandizani kudziŵa mwamsanga zocitika m’nthawi ya Esitere ndi ubwino wa buku limeneli. Bukuli lionetsa mmene Esitere anacitila zinthu molimba mtima kuti ateteze anthu a Mulungu.