Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Baibulo

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Baibulo

M’Baibulo, Mulungu amadzidziwikitsa yekha kuti iye ndi Mlengi, amafotokoza cholinga chake choti zolengedwa zonse zanzeru zidzakhale ndi moyo mpaka kalekale komanso amatchula dzina lake lenileni, lakuti Yehova.