Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Nkhani Zokhudza Zachipatala Zimene Zingathandize Madokotala

Nkhani zimene akatswiri ena a zachipatala analemba, zikusonyeza kuti anthu ambiri analandira thandizo la mankhwala komanso kupangidwa maopaleshoni ovuta popanda kuikidwa magazi athunthu kapena zigawo zikuluzikulu za magaziwo. Kuti munthu asaikidwe magazi, pamafunika kuti madokotala agwiritse ntchito njira zosiyanasiyana kuti athandize wodwala kuti asataye magazi ambiri, kuti thupi lake lizipanga magazi komanso kuti agwiritse ntchito bwino magazi a wodwala pa nthawi ya opaleshoni. Chigawo chino chikuthandizani kudziwa mfundo zofufuzidwa bwino zochokera m’magazini odziwika ofotokoza zachipatala zimene zikupereka umboni wosonyeza kuti n’zotheka kugwiritsa ntchito magazi a wodwala pomupanga opaleshoni komanso kugwiritsa ntchito njira zina popanda kumuika magazi.

 

Featured Articles

Uterine packing with chitosan-covered tamponade to treat postpartum hemorrhage. (imatsegula tsamba lina)

Henrich W, Dückelmann A, Braun T, Hinkson L

Source‎: Am J Obstet Gynecol 2024;230(3S):S1061-65.

Indexed‎: PubMed 38462249

DOI‎: 10.1016/j.ajog.2022.11.1297

https://pubmed.ncbi.nlm.nih.gov/38462249/ (imatsegula tsamba lina)