Onani zimene zilipo

Cibwenzi

Mukayang’ana kulikonse, mumaona anthu amene ali pacibwenzi. Kodi ndinu wokonzeka kukhala pacibwenzi? Ngati ndinu wokonzeka, kodi mungacite ciyani kuti mupewe zinthu zimene zingakubweletseleni mavuto? Nanga mungasankhe bwanji zinthu mwanzelu kuti mukakhale na banja lacimwemwe mtsogolo?

Pamene Muli Pacibwenzi

Ndi Cikondi Ceni-ceni Kapena Kutengeka Maganizo Cabe?

Tambani vidiyoyi kuti mudziŵe tanthauzo la kutengeka maganizo ndiponso cikondi ceniceni.