Pitani ku nkhani yake

Kugonana

Kugonana pakokha si kolakwika, komabe timafunika kulamulira zilakolako zathu. Kodi mungakwanitse bwanji kukhala odziletsa popeza kuti m’dzikoli anthu ambiri amakonda zachiwerewere?

Kuchitiridwa Nkhanza

Kodi Ndizitani Ngati Ena Akundichitira Zachipongwe?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe tanthauzo la kuchitiridwa zachipongwe komanso zimene mungachite ngati mutachitiridwa zachipongwezo.

Zimene Achinyamata Amanena pa Nkhani ya Nkhanza Zokhudza Kugonana

Onani zimene achinyamata 5 ananena pa nkhani yochitiridwa nkhanza zokhudza kugonana komanso zimene mungachite wina akakuchitirani nkhanzazo.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Nkhanza za Kugonana?—Gawo 1: Mmene Mungadzitetezere

Pali njira zitatu zimene zingakuthandizeni kuti mupewe kuchitidwa nkhanza zokhudza kugonana.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Nkhanza za Kugonana?​—Gawo 2: Zimene Mungachite Ngati Munachitidwapo Nkhanza Zotere

Werengani zimene zinathandiza anthu omwe anachitidwa nkhanza zokhudza kugonana kuti azikhala osangalala.

Zimene Baibulo Limanena

Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana?

Ngati mutafunsidwa kuti: ‘Kodi sunagonanepo ndi munthu chibadwire?’ kodi mungathe kugwiritsa ntchito Baibulo poyankha?

Mmene Mungafotokozere Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana

Nthawi zina aliyense amafunika kufotokoza zimene amakhulupirira. Gwiritsani ntchito nkhani yakuti “Zoti Muchite,” pokonzekera mmene mungafotokozere zimene mumakhulupirira molimba mtima.

Kodi Kugonana M’kamwa Kumakhaladi Kugonana?

Kodi mtsikana akhoza kutenga mimba chifukwa chogonana m’kamwa?

Kodi Kugonana Kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha N’kolakwika?

Kodi Baibulo limanena kuti anthu amene amagonana ndi amuna kapena akazi anzawo ndi oipa? Kodi Mkhristu akhoza kukhala paubwenzi ndi Mulungu ngakhale atamakhala ndi chilakolako chofuna kugonana ndi amuna kapena akazi anzake?

Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Kukambirana nkhani ngati izi kumakhala kovuta. Tsambali lingakuthandizeni kuti muzifotokoza mwanzeru komanso mosamala maganizo anu pa nkhani ya kugonana kwa amuna kapena akazi okhaokha.

Kukhalabe ndi Khalidwe Labwino

Ndingatani Ngati Anzanga Akundikakamiza Kugonana?

Onani zimene anthu ena amakhulupirira komanso zoona zake pa nkhani ya kugonana. Nkhaniyi ikuthandizani kuti musankhe zinthu mwanzeru.

Ndingatani Ngati Anzanga Akundikakamiza Kuti Ndichite Zachiwerewere?

Pali mfundo zitatu za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni kukana mayesero.

Ndingatani Kuti Ndisamangoganizira Zogonana?

Kodi mungatsatire mfundo ziti ngati mutayamba kuganizira zogonana?

Kodi ndi Bwino Kulonjeza Kuti Ndikhala Wodzisunga Mpaka Ndidzalowe M’banja?

Kodi kuchita zimenezi kungathandizedi kupewa zogonana musanalowe m’banja?

Muziganizira Kufunika kwa Zomwe Mumakhulupirira: Pa Nkhani ya Kudzisunga

Tsambali lingakuthandizeni kuti muzisankha mwanzeru ngakhale zinthu zitavuta.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?

Kodi munthu wina amakukakamizani kuti mumutumizire zolaula? Kodi kutumizirana zolaula kuli ndi mavuto otani? Kodi ndi kukopana basi?

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula?

Kodi kuonera zolaula n’kofanana motani ndi kusuta fodya?

Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula

N’chifukwa chiyani pulogalamu yoteteza kuonera zolaula pa Intaneti siyokwanira?

Kodi Mukulephera Kusiya Kuonerera Zinthu Zolaula?

Baibulo lingakuthandizeni kuti mumvetse cholinga cha zinthu zolaula.

Pewani Kulakalaka Zinthu Zoipa

Chitani zimene mwauzidwa kuti muchite, ndipo mukamawerenga nkhani ya m’Baibuloyi ya Davide ndi Bati-seba, muziyerekezera kuti mukuona zimene zikuchitikazo. Kodi tingaphunzirepo chiyani pa nkhaniyi?

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa?

Onani zinthu zitatu zimene zingakuthandizeni kuti musamagonje mukayesedwa.

Mungatani Kuti Musamagonje Mukakumana ndi Mayesero?

Mwamuna komanso mkazi weniweni amatha kupewa mayesero. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 6 zimene zingakuthandizeni kusagonja mukamayesedwa komanso kuti musakhale ndi nkhawa chifukwa chodziwa kuti mwagonja.

Zimene Mungachite Kuti Muzipewa Mayesero

Pamene Yosefe ankayesedwa kuti achite chigololo, kodi n’chiyani chinamuthandiza kuti achite zinthu zoyenera?