Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

3-A

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 1)

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 1)

Mafumu a mu Ufumu Wakum’mwera wa Mafuko Awiri a Yuda

997 B.C.E.

Rehobowamu: zaka 17

980

Abiya (Abiyamu): zaka zitatu

978

Asa: zaka 41

937

Yehosafati: zaka 25

913

Yehoramu: zaka 8

M’ma 906

Ahaziya: chaka chimodzi

M’ma 905

Mfumukazi Ataliya: zaka 6

898

Yehoasi: zaka 40

858

Amaziya: zaka 29

829

Uziya (Azariya): zaka 52

Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto wa Mafuko 10 a Isiraeli

997 B.C.E.

Yerobowamu: zaka 22

M’ma 976

Nadabu: zaka ziwiri

M’ma 975

Basa: zaka 24

M’ma 952

Ela: zaka ziwiri

Zimiri: masiku 7 (cha m’ma 951)

M’ma 947

Omuri ndi Tibini: zaka 4

Omuri (yekha): zaka 8

M’ma 940

Ahabu: zaka 22

M’ma 920

Ahaziya: zaka ziwiri

M’ma 917

Yehoramu: zaka 12

M’ma 905

Yehu: zaka 28

876

Yehoahazi: zaka 14

M’ma 862

Yehoahazi ndi Yehoasi: zaka zitatu

M’ma 859

Yehoasi (yekha): zaka 16

M’ma 844

Yerobowamu Wachiwiri: zaka 41

  • Mayina a Aneneri

  • Yoweli

  • Eliya

  • Elisa

  • Yona

  • Amosi