Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

4-G

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu M’Yerusalemu (Gawo 1)

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu M’Yerusalemu (Gawo 1)

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

33, Nisani 8

Betaniya

Afika ku Betaniya masiku 6 Pasika asanachitike

     

11:55–12:1

Nisani 9

Betaniya

Mariya amuthira Yesu mafuta m’mutu ndi m’mapazi

26:6-13

14:3-9

 

12:2-11

Betaniya-Betefage-Yerusalemu

Alowa m’Yerusalemu monga wopambana, atakwera bulu

21:1-11, 14-17

11:1-11

19:29-44

12:12-19

Nisani 10

Betaniya-Yerusalemu

Atemberera mkuyu wosabereka; athamangitsanso ogulitsa malonda pa kachisi

21:18, 19; 21:12, 13

11:12-17

19:45, 46

 

Yerusalemu

Ansembe aakulu ndi alembi akonza chiwembu kuti aphe Yesu

 

11:18, 19

19:47, 48

 

Mawu a Yehova amveka; Yesu aneneratu za imfa yake; kusakhulupirira kwa Ayuda kukwaniritsa ulosi wa Yesaya

     

12:20-50

Nisani 11

Betaniya-Yerusalemu

Mkuyu wosabereka aupeza utauma

21:19-22

11:20-25

   

Yerusalemu, m’kachisi

Akayikira ulamuliro wa Khristu; fanizo la ana aamuna awiri

21:23-32

11:27-33

20:1-8

 

Mafanizo a olima munda oipa, ndi phwando la ukwati

21:33–22:14

12:1-12

20:9-19

 

Amufunsa mafunso okhudza Mulungu ndi Kaisara, kuuka kwa akufa, ndi lamulo lalikulu kuposa onse

22:15-40

12:13-34

20:20-40

 

Yesu afunsa anthu ngati Khristu ali m’mzera wobadwira wa Davide

22:41-46

12:35-37

20:41-44

 

Adzudzula mwamphamvu alembi ndi Afarisi

23:1-39

12:38-40

20:45-47

 

Kakhobidi ka mkazi wamasiye

 

12:41-44

21:1-4

 

Phiri la Maolivi

Anena chimene chidzakhale chizindikiro cha kukhalapo kwake

24:1-51

13:1-37

21:5-38

 

Mafanizo a anamwali 10, matalente, nkhosa ndi mbuzi

25:1-46

     

Nisani 12

Yerusalemu

Atsogoleri Achiyuda akonza zopha Yesu

26:1-5

14:1, 2

22:1, 2

 

Yudasi akambirana ndi ansembe zoti amupereke Yesu

26:14-16

14:10, 11

22:3-6

 

Nisani 13 (Lachinayi masana)

Pafupi ndi Yerusalemu, ndi mkati mwake

Akonzekera Pasika yomaliza

26:17-19

14:12-16

22:7-13

 

Nisani 14

Yerusalemu

Adya chakudya cha Pasika pamodzi ndi atumwi

26:20, 21

14:17, 18

22:14-18

 

Asambitsa mapazi a atumwi ake

     

13:1-20