Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

16-A

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1)

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1)

Nisani 8 (Sabata)

KULOŴA KWA DZUŴA Masiku Aciyuda anali kuyamba ndi kutha poloŵa dzuŵa

  • Afika ku Betaniya masiku 6 Pasika asanacitike

  • Yohane 11:55–12:1

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 9

KULOŴA KWA DZUŴA

  • Akudya ndi Simoni wakhate

  • Mariya adzoza Yesu ndi nado

  • Ayuda abwela kudzaona Yesu ndi Lazaro

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Aloŵa m’Yerusalemu monga mfumu

  • Aphunzitsa m’kacisi

KULOŴA KWA DZUŴA]

Nisani 10

KULOŴA KWA DZUŴA]

  • Agona ku Betaniya

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Alaŵilila ku Yerusalemu

  • Ayeletsa kacisi

  • Yehova alankhula kucokela kumwamba

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 11

KULOŴA KWA DZUŴA

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Aphunzitsa m’kacisi, pogwilitsila nchito mafanizo

  • Adzudzula Afalisi

  • Aona copeleka ca mkazi wa masiye

  • Paphili la Maolivi, anenelatu mmene Yerusalemu adzagwela ndi kupeleka zizindikilo za kukhalapo kwake mtsogolo

KULOŴA KWA DZUŴA