18-B
Ndalama ndi Muyezo
Ndalama ndi Muyezo m’Malemba Aciheberi
Gera (sekeli 1⁄20) Magalamu 0.57 / Maonsi 0.01835 Magera 10 = Beka 1 |
Beka Magalamu 5.7 / Maonsi 0.1835 Mabeka 2 = Sekeli 1 |
Pimu Magalamu 7.8 / Maonsi 0.2508 Pimu 1 = Sekeli 2⁄3 |
Sekeli Magalamu 11.4 / Maonsi 0.367 Sekeli 50 = Mina 1 |
Mina magalamu 570 / Maonsi 18.35 Mamina 60 = Talente 1 |
Talente Makilogalamu 34.2 / Maonsi 1,101 |
Dariki (Golide wa ku Perisiya) Magalamu 8.4 / Maonsi 0.27 Ezara 8:27 |
Ndalama ndi Muyezo m’ma Malemba Acikristu Acigiliki
Leputoni (Mkuwa kapena bronzi yaciyuda) Makuadirani 1⁄2 Luka 21:2 |
Makuadirani (Mkuwa kapena bronzi yaciroma) Maleputa 2 |
Asariyoni (Mkuwa kapena bronzi yaciroma ndi zigawo) Makuadiranti 4 |
Dinari (Siliva yaciroma) Makuadiranti 64 Magalamu 3.85 / Maonsi 0.124 Malipilo a Tsiku Limodzi (Maola 12) |
Dirakima (Siliva yacigiriki) Magalamu 3.4 / Maonsi 0.109 Luka 15:8 Malipilo a Tsiku Limodzi (Maola 12) |
Madirakima (Siliva yacigiriki) Madirakima 2 Magalamu 6.8 / Maonsi 0.218 Malipilo a Masiku Aŵili |
Matetiradirakima (Siliva yacigiriki; yochedwanso kobidi ya golide kapena siliva) Madirakima 4 Magalamu 13.6 / Maonsi 0.436 Malipilo a Masiku anai |
Mina Madalakima 100 Magalamu 340 / Maonsi 10.9 Luka 19:13 = pafupifupi 100 malipilo atsiku limodzi |
Talente Mamina 60 Makilogalamu 20.4 / Maonsi 654 Chivumbulutso 16:21 = pafupifupi malipilo azaka 19 |
Paundi (Yaciroma) Magalamu 327 / Maonsi 11.5 Yohane 12:3
|