Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mwana Wamkazi Wokondedwa

Mwana Wamkazi Wokondedwa

Daunilodi:

  1. 1.Iwo anaona

    Ali mwana.

    Inde ni zambili

    Adzapitamo.

    Koma iye anaŵakondweletsa

    Popilila ziyeso.

    (KOLASI)

    Iwe mwana, akunyadila.

    Nthawi zonse akukonda.

  2. 2.Niwodzipeleka

    Nthawi zonse.

    Zonse amuuza

    Amatsatila.

    Ndipo amakondwela

    Akamvela

    Atate wake akuti;

    (KOLASI)

    “Mwana wanga wamkazi iwe,

    Nthawi zonse n’dzakukonda.”

    (BILIJI)

    Yehova M’lungu adziŵa zonse,

    Ndiponso khama unaonetsa.

    Sadzaiŵala cikondi cako

    Pom’tamanda.

    (KOLASI)

    Iwe mwana akunyadila.

    Nthawi zonse sadzakusiya.

    M’lungu adzakusamalila.

    Iye amakukonda.