Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tiyamikila

Tiyamikila

Daunilodi:

  1. 1. Nikavutika

    Mumaganizo

    Mumamvela

    Niyamikila.

  2. 2. Tikavutika

    Mutithandiza

    Mumayankha

    Tiyamikila.

  3. 3. Tisadele nkhawa

    Za ciliconse

    Mudzatithandiza.

    Ngati tipitiliza kudalila

    Inu nthawi zonse.

  4. 4. Pa zinthu zonse

    Muthandiza

    Tiyamikila.

  5. 5. Mumakonda okukondani

    M’zinthu zonse tiyamikila.