Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Nidzasinthadi

Nidzasinthadi

Daunilodi:

  1. 1. Nimaganizila

    Utumiki

    Wanga kwa Yehova,

    Supita patsogolo

    Zinthu nikuchitazi

    Sizisintha.

    Lomba nikufunika cabe

    Niwonjezeleko.

    (KOLASI)

    Kuyambila lelo nidzasinthadi

    Utumiki wanga udzasintha.

    Yehova M’lungu nadziwa

    Kuti kudalila imwe ningasinthedi.

  2. 2. Nikalimba mtima nidzaona

    Kuti kusinthaku

    Kudzanitsitsimula

    Kusintha zinthu

    Kunipatsa mphamvu

    Sininali kuona

    Kuti zitseko n’zotseguka.

    (KOLASI)

    Kuyambila lelo nidzasinthadi

    Utumiki wanga udzasintha.

    Yehova M’lungu nadziwa

    Kuti kudalila imwe ningasinthedi.

    (BILIJI)

    Zinali kuoneka monga

    Sizingatheke

    Sininali kudziwa cifukwa cake.

    Kulimba mtima nakupitabe patsogolo,

    Kuleta madalitso lelo na mtsogolo.

    (KOLASI)

    Tsiku iliyonse nidzasinthabe

    Utumiki wanga ukusintha

    Yehova n’nadziwadi zocita

    Ninakudalilani Munan’dalitsa.

    (KOLASI)

    Kuyambila lelo nidzasinthadi

    Utumiki wanga udzasintha.

    Yehova M’lungu nadziŵa

    Kuti kudalila imwe.

    (KOLASI)

    Kuyambila lelo nidzasinthadi

    Utumiki wanga udzasintha.

    Yehova M’lungu nadziŵa

    Kuti kudalila imwe ningasinthedi.