Tisaope YAMBANI Tisaope Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu 1. Timakumana ndi zokhoma ndithu. Timakhumudwa ndimavutowa. Tikasowatu chochita, Tisamataye mtima. M’lungu Alipo. (KOLASI) Tisaope iye alipo, Atithandiza ndi dzanja lakelo. Pomwe zinthu zavuta, Tisaiwale sitili tokha. Tizimupemphatu Kuti Tisamaope. 2. Mwatithandiza kupeza ‘nzathu. Amatipempherera pomwe zavuta. Mawu anu athandiza Kuti tizipirirabe Mavuto, N’zotheka. (KOLASI) Tisaope iye alipo, Atithandiza ndi dzanja lakelo. Pomwe zinthu zavuta, Tisaiwale sitili tokha. Tizimupemphatu Ndithu. (VESI LOKOMETSERA) Tikakumana ndi mavuto, Tipirire. Zidzayenda. (KOLASI) Tisaope iye alipo, Atithandiza ndi dzanja lakelo. Pomwe zinthu zavuta, Tisaiwale sitili tokha. Tizimupemphatu Kuti Tisamaope. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Tisaope NYIMBO ZATHU Tisaope Chinenero Chamanja cha ku Malawi Tisaope https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014252/univ/art/1014252_univ_sqr_xl.jpg