Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Uzidekha

Uzidekha

Mawu a Nyimbo:

  1. 1. Poyenda uzidekha,

    Inde n’zovuta kuziletsa.

    Ngati uli na mabwenzi,

    Kuno simalo ya maseŵela.

    (KOLASI)

    Uzidekha

    Ucite zinthu bwino.

    Ukonde nchito yako

    Uzidekha.

  2. 2. Zocita ni zambili,

    Mpingo wonse ukudalila.

    Kumbukila abale,

    Uŵakonde nakuceza nawo.

    (KOLASI)

    Uzidekha

    Ucite zinthu bwino.

    Ukonde nchito yako

    Uzidekha

  3. 3. Ungafike panyumba

    Kodi alipo olo palibe?

    Udziona ali pafupi

    Ukambenso na oyenda mu njila.

    (KOLASI)

    Uzidekha

    Ucite zinthu bwino.

    Ukonde nchito yako

    Uzidekha.

    Uzidekha.