Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu YAMBANI Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Kusanache, Wadzukatu Akupempherera Ana ake ndi Abale onse: “Tate, tithandizeni.” Zinthu zikamavuta, Amakhalabe wolimba, N’ngokoma mtima. Nyimbo iyi amaikonda: (KOLASI) ‘N’dzakulimbitsa. Usaopetu. N’dzakhala nawe. N’dzakuthandiza.’ Ulimbetu mtima. Nyimbo yokondedwa: “Adzakulimbitsa, Adzakuteteza.” (VESI LOKOMETSERA) Akugwira ntchito Sizophwekadi Sakudziwa zamawa Anzakewatu Amamukondadi Moti sadandaula 2. M’lungu amam’patsa mphamvu Ndipotu safo’ka. Amachita khama kugwira ntchito— Amapemphera mumtima Atatopa kwambiri— Mayiyu akuyesetsa. Nyimbo ija amaikonda Imam’limbikitsa. (KOLASI) ‘N’dzakulimbitsa. Usaopetu. N’dzakhala nawe. N’dzakuthandiza.’ Ulimbetu mtima. Nyimbo yokondedwa: “Adzakulimbitsa, Adzakuteteza.” “Adzakulimbitsa, Adzakuteteza.” Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu NYIMBO ZATHU Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014307/univ/art/1014307_univ_sqr_xl.jpg