Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ndadzipereka Kwa Inu

Ndadzipereka Kwa Inu

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Usiku kuli bata,

    Nyenyezi zikuwala,

    Ndikaganiza za ntchito zanu,

    Ndimakukondani.

  2. 2. Ndikadziperekatu,

    Mudzanditsogolera.

    Masiku akamadutsa ndithu

    Ndidzakhulupirika.

    (KOLASI)

    Chikhulupiriro

    Chathandiza

    Kuti ndipirire,

    Mwapereka dipo

    Mwana wanu,

    Ndadziperekadi;

    Ndadziperekadi.

  3. 3. Mmene dzuwa lawala,

    Ndamvatu kutenthera,

    M’matidalitsa tsiku ndi tsiku

    Ndimayamikiradi.

    (KOLASI)

    Chikhulupiriro

    Chathandiza

    Kuti ndipirire,

    Mwapereka dipo

    Mwana wanu,

    Ndadziperekadi;

    Ndadziperekadi.

    (KOLASI)

    Chikhulupiriro

    Chathandiza

    Kuti ndipirire,

    Mwapereka dipo

    Mwana wanu,

    Ndadziperekadi;

    Ndadziperekadi.