Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

M’sakaikile

M’sakaikile

Daunilodi:

  1. 1. Mumapemphela, nolalikila

    Ndimwenso wokhulupilika

    Sitiona zimene mupitamo

    Koma Yehova amaona.

    (MWANA WA KOLASI)

    Conco mukaimilila mu khoti

    Simuli mwekha.

    Ndimwedi citsanzo kwa tonse

    Limbani mtima.

    (KOLASI)

    Natsimikiza

    Kuti palibe cingatilekanitse

    Na Yehova.

    Ngakhale imfa

    Kaya moyo na maboma

    Sizidzatilekanitsa.

    M’sakaikile,

    M’lungu atikonda.

  2. 2. M’mavuto onse simumafo’ka

    Mumadalila Yehova M’lungu,

    Ngakhale adani akuletseni

    Kulalikila simuleka.

    (MWANA WA KOLASI)

    Conco mukaimilila mu khoti,

    Simuli mwekha.

    Ndimwedi citsanzo kwa tonse

    Limbani mtima.

    (KOLASI)

    Natsimikiza

    Kuti palibe cingatilekanitse

    Na Yehova.

    Ngakhale imfa

    Kaya moyo na maboma

    Sizidzatilekanitsa.

    M’sakaikile,

    M’lungu atikonda.

    Oo!

    Atikonda

    Oo! oo! oo! oo!

    (BILIJI)

    M’saiŵale

    Kuti muvutika cifukwa

    Ca M’lungu wanu,

    Ndipo imwe mudzapambanadi

    Olo zivute.

    Mudzapambana.

    (KOLASI)

    Natsimikiza

    Kuti palibe cingatilekanitse

    Na Yehova.

    Ngakhale imfa

    Kaya moyo na maboma

    Sizidzatilekanitsa.

    Natsimikiza

    Kuti palibe cingatilekanitse

    Na Yehova.

    Ngakhale imfa

    Kaya moyo na maboma

    Sizidzatilekanitsa.

    M’sakaikile

    M’lungu atikonda.