Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ndiwe Wekha

Ndiwe Wekha

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Ndiwetu

    Munthu wapadera.

    Inetu

    Ndimakukonda.

    Makhalidwe ako

    Aman’sangalatsa.

    Yehovatu

    Adzatidalitsa.

    Ndimamvatu bwino

    Umandithandiza.

    Ndiwe waulemu

    Umandikondadi.

    (KOLASI)

    Tikamagwirizana

    Chikondi chimakula.

    Tithokoze M’lungu, timakondana.

    Ndiwe wekha.

  2. 2. Wanga ndiwe wekha.

    Umandimvetsera.

    Limodzitu,

    Timalalikira.

    Ndimamvatu bwino

    Umandikondadi.

    Ulipotu wekha—

    Ndimasangalala.

    (KOLASI)

    Tikamagwirizana

    Chikondi chimakula.

    Tithokoze M’lungu, timakondana.

    Ndiwe wekha.

    Tikamagwirizana

    Chikondi chimakula.

    Tithokoze M’lungu, timakondana.

    Ndiwe wekha,

    Ndiwe wekha,

    Wanga.