Ndikhululuke YAMBANI Ndikhululuke Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Chakukhosi ndachisungadi. Chikulemera, ndafooka. Ndikuyenera kusintha. Ndifunika kukhululuka. N’zovuta ngati wolakwa si ‘ne. N’ngavutike kukhululuka. (KUKONZEKERA KOLASI) Ndipempheretu ndipo n’sachedwe. Yehova akudziwa chilichonse. Wandipatsadi mphamvu (KOLASI) Kuti mpirire. Sin’ngakwanitse pandekha. Chonde M’lungu thandizeni Kuti n’khululuke. Nditsanzire M’lungu Pokhululuka, ndi kuiwala. Chonde M’lungu thandizeni Kuti n’khululuke. N’khululuke. 2. Ndayesetsa kuziiwala, Pena mmakumbukila. N’kanakonda kungoziiwala. Ndiiwale n’kakhululuka. Ukutu ndiye kukhululukadi. Moyo upitirirebe. (KUKONZEKERA KOLASI) Ndipempheretu ndipo n’sachedwe. Yehova akudziwa chilichonse. Wandipatsadi mphamvu (KOLASI) Kuti mpirire. Sin’ngakwanitse pandekha. Chonde M’lungu thandizeni Kuti n’khululuke. Nditsanzire M’lungu Pokhululuka, ndi kuiwala. Chonde M’lungu thandizeni Kuti n’khululuke. N’khululuke. N’khululuke. N’khululuke. N’khululuke. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ndikhululuke NYIMBO ZATHU Ndikhululuke Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndikhululuke https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014337/univ/art/1014337_univ_sqr_xl.jpg