Sitisiya YAMBANI Sitisiya Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Nditamva cho’nadi koyamba Za Yehova ndi za paradaiso, N’nayamba kuzikonda kwambiri. M’dzikoli zosokoneza n’zambiri. (KUKONZEKERA KOLASI) Sindingasiye, N’zichita zoyenera. (KOLASI) Ndikulimbitsa chikhulupiriro. Sindidzabwerera m’mbuyo. Mawu ake anditsogolere. Ndikupempha ndipirire. Ndikhale wolimba, sindisiya. 2. Tikhozatu kusankha mwanzeru Polimbitsa chikhulupiriro. Dzikoli likufuna tisinthe Ndikumachita zomwe tikufuna. (KUKONZEKERA KOLASI) Posachedwatu, Dziko likupita. (KOLASI) Tikulimbitsa chikhulupiriro. Sitidzabwerera m’mbuyo. Mawu ake atitsogolere. Tikupempha tipirire. Tikhale olimba, sitisiya. (KOLASI) Tikulimbitsa chikhulupiriro. Sitidzabwerera m’mbuyo. Mawu ake atitsogolere. Tikupempha tipirire. Tikhale olimba, sitisiya. Sitisiya. Sitisiya. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Sitisiya NYIMBO ZATHU Sitisiya Chinenero Chamanja cha ku Malawi Sitisiya https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014338/univ/art/1014338_univ_sqr_xl.jpg