Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Cimwemwe Cathu Camuyaya

Cimwemwe Cathu Camuyaya

(Salimo 16:11)

Daunilodi:

  1. 1. Kumwamba kuli nyenyezi ndipo ziwala.

    Munakongoletsa usana na usiku.

    Manja anu anapanga zinthu zonse,

    Mukondwela mukaziona.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga waufumu,

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha,

    Ndiye cuma camuyaya

    Ndimwe cimwemwe cathu.

    Inde, ca muyaya.

  2. 2. Yehova tili na zonse zosangalatsa.

    Zonse tiona na maso, zikhudza mtima.

    Mwatipatsa umuyaya,

    Mumitima yathu na cimwemwe cosatha.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga waufumu,

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha,

    Ndiye cuma camuyaya

    Ndimwe cimwemwe cathu.

    Inde, ca muyaya.

    (BILIJI)

    Munapeleka Yesu

    Kuti atifele

    Sitikanapeza cimwemwe

    Popanda nsembe yake.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga waufumu,

    Zimatikondweletsa.

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya.

    Ndimwe cimwemwe cathu

    Inde, ca muyaya.

    (KOLASI)

    Cilengedwe canu M’lungu

    Na uthenga waufumu,

    Zimatikondweletsa

    Cikondi canu cosatha

    Ndiye cuma camuyaya

    Ndimwe cimwemwe cathu

    Inde, ca muyaya.

(Onaninso Sal. 37:4; 1 Akor. 15:28.)