Ndi Maso a Chikhulupiriro YAMBANI Ndi Maso a Chikhulupiriro Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Salimo 27:13) Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Ndioperenji mkango? Ndioperenji anthu? Yehovatu alipo Ndiopenso chani! M’lungu andipulumutsa. (KOLASI) Ndi masotu a chikhulupiriro Sindidzaopa chilichonsecho. Yehovatu alipo Sindichita mantha, Amakhala nane pafupi An’thandiza. 2. Atumiki akale Anakhulupirika. Chikhulupiriro Chinawathandiza. M’lungu adzawaukitsa. (KOLASI) Ndi masotu a chikhulupiriro Sindidzaopa chilichonsecho. Yehovatu alipo Sindichita mantha, Amakhala nane pafupi An’thandiza. (VESI LOKOMETSERA) Ndi Yehova, zonse ndi zotheka Ndili n’chikhulupiriro. Chikhulupiriro chathandiza kuti Ndipirire pa mavuto. 3. M’lungu wandilonjeza Tsogolo labwino. Ndipirirebe Poti posachedwa Yehova athetsa mavuto. (KOLASI) Ndi masotu a chikhulupiriro Sindidzaopa chilichonsecho. Yehovatu alipo Sindichita mantha, Amakhala nane pafupi An’thandiza. An’thandiza. (Onaninso Aheb. 11:1-40.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ndi Maso a Chikhulupiriro NYIMBO ZATHU Ndi Maso a Chikhulupiriro Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndi Maso a Chikhulupiriro https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014354/univ/art/1014354_univ_sqr_xl.jpg