Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Pamodzi, Timalimba Mtima

Pamodzi, Timalimba Mtima

Pangani Dawunilodi:

  • (MAWU OYAMBIRA)

    Moni abale nonsenu!

    Uthengawu ndi wanu!

  1. 1. Tonse timakondana

    Ngakhale tisiyane mtundu.

    Zomwe timaphunzira

    N’zofananansotu kulikonse.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Mukakumana

    N’zothetsa nzeru

    Dziwani simuli nokha.

    (KOLASI)

    Limodzi, nonsenu tilitu limodzi.

    Limodzi, tonsefe tipirire ndithu.

    Limodzi, pamodzi, timagwirizana.

    Timakondana zedi, pamodzi timalimba mtima.

  2. 2. Tili m’mayiko onse.

    Zikhalidwe n’zosiyanadi.

    Tingasiyane mtundu,

    Koma timakondana kwambiri.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Kulikonseko

    Padziko lonse

    Timakondana kwambiri.

    (KOLASI)

    Limodzi, nonsenu tilitu limodzi.

    Limodzi, tonsefe tipirire ndithu.

    Limodzi, pamodzi, timagwirizana.

    Timakondana zedi, pamodzi timalimba mtima.

    Limodzi, tonsefe pamodzi.

    (KOLASI)

    Limodzi, nonsenu tilitu limodzi.

    Limodzi, tonsefe tipirire ndithu.

    Limodzi, pamodzi, timagwirizana.

    Timakondana zedi, pamodzi timalimba mtima.

    Timalimba mtima.

    Timalimba mtima.