Kudzakhala Mtendere (Nyimbo ya Msonkhano ya 2022) YAMBANI Kudzakhala Mtendere (Nyimbo ya Msonkhano ya 2022) Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Pomwe dziko likusowa mtendere Ife tili ndi mtendere. Sitida nkhawa Chifukwa Yehova Adzathetsatu mavuto. (KOLASI) Padziko lapansi Padzakhalatu Mtendere wosatha. Mavuto akatha, Tidzapumula. Konse kudzakhala Mtendere. 2. Tikalowa m’dziko Latsopano Moyo udzasangalatsa. Mtendere womwe Tikulakalaka Yehova adzatipatsa. (KOLASI) Padziko lapansi Padzakhalatu Mtendere wosatha. Mavuto akatha, Tidzapumula. Konse kudzakhala Mtendere. (KOLASI) Padziko lapansi Padzakhalatu Mtendere wosatha. Mavuto akatha, Tidzapumula. Tidzasangalala! (KOLASI) Padziko lapansi Padzakhalatu Mtendere wosatha. Mavuto akatha, Tidzapumula. Konse kudzakhala Mtendere, Mtendere! Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kudzakhala Mtendere (Nyimbo ya Msonkhano ya 2022) NYIMBO ZATHU Kudzakhala Mtendere (Nyimbo ya Msonkhano ya 2022) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kudzakhala Mtendere (Nyimbo ya Msonkhano ya 2022) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014367/univ/art/1014367_univ_sqr_xl.jpg