Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Moyo Wosatha

Moyo Wosatha

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. M’dzikoli ndi zovuta

    Kuti usiyanitse

    Zabwinotu ndi zoipa.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Komatu Yehova akuti: ‘Pewa nzeru za dziko’.

    Upeza moyo wosathadi.

    (KOLASI)

    Pirira, pemphera.

    Yehova ali nawe, sulitu wekha.

    Ndiye limbabe.

    Mavuto angakule, akuthandiza.

    Ganiza za moyo, moyo wosatha.

  2. 2. Dzikoli likufuna

    Ukhale wodziwika

    Kwa anthu, utchuketu.

    (KUKONZEKELA KOLASI)

    Koma ndi zachabechabe, ndi kuthamangitsa mphepo.

    Ndiye ganiza za mtsogolo.

    (KOLASI)

    Pirira, pemphera.

    Yehova ali nawe, sulitu wekha.

    Ndiye limbabe.

    Mavuto angakule akuthandiza.

    Ganiza za moyo, moyo wosatha

    (KOLASI)

    Pirira, pemphera.

    Yehova ali nawe, sulitu wekha.

    Ndiye limbabe.

    Mavuto angakule, akuthandiza.

    Ganiza za moyo, moyo wosatha.