“Sadzachedwa” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2023) YAMBANI “Sadzachedwa” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2023) Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu (Habakuku 2:3) 1. Dziko lopanda nkhawa zonsezi Ndi lomwe tonse tikulakalaka. Padziko lonse zinthu zaipa Tikudziwatu muthetsa zonsezi. (KOLASI) Molezadi mtima tikudikirira Dzikotu latsopano. Mapeto afika posachedwa pompa. Mawu anu akuti, ‘sadzachedwadi.’ 2. Mulungu wathu mudzaitana Omwe anafa, ndipo adzadzuka. Zidzakhalatu zosangalatsa! Tithandizeni kulezabe mtima. (KOLASI) Molezadi mtima tikudikirira Dzikotu latsopano. Mapeto afika posachedwa pompa. Mawu anu akuti, ‘sadzachedwadi.’ 3. Mumafufuza mitima yathu N’kutitonthoza ndi chiyembekezo. Tichite khama polalikira. Tikhale maso nthawi yafupika. (KOLASI) Molezadi mtima tikudikirira Dzikotu latsopano. Mapeto afika posachedwa pompa. Mawu anu akuti, ‘sadzachedwadi.’ Tiyembekezerebe. (Onaninso Akol. 1:11.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena “Sadzachedwa” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2023) NYIMBO ZATHU “Sadzachedwa” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2023) Chinenero Chamanja cha ku Malawi “Sadzachedwa” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2023) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014381/univ/art/1014381_univ_sqr_xl.jpg