Tisafooke

Tisafooke
  1. 1. Nthawi yafupika

    Dziko liwonongedwa.

    Koma anthu adziwa bwanji?

    Tiwalalikire.

  2. 2. Tisakhale chete.

    Tisamachite mantha.

    Tidaliretu M’lungu wathu

    Azitithandiza.

    (KOLASI)

    Ngati moto woyaka

    Tizilalikira.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisamanyalanyaze

    Tidziwitse onse.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisafo’ke.

  3. 3. Tizichita khama.

    Nthawiyi yafupika.

    Tiliyeretse dzina lake.

    Tidzasangalala.

    (KOLASI)

    Ngati moto woyaka

    Tizilalikira.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisamanyalanyaze

    Tidziwitse onse.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisafo’ke.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Moto uziyakatu mumtima mwathu.

    Tsiku la Yehova likubwera

    Posachedwa.

    (KOLASI)

    Ngati moto woyaka

    Tizilalikira.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisamanyalanyaze

    Tidziwitse onse.

    Inde! Tisafo’ke.

    Tisafo’ke.

    Tisafo’ke.

    Tisafo’ke.