“M’dziko Labwino” YAMBANI “M’dziko Labwino” Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu 1. Moyo wabwino, ngati kutulo, tili m’dziko labwino. Imfa yagonja nkhawa zonse zatha! Takhalanso angwiro. Zonse zomwe tikuona, n’zosangalatsa. Yehova watipatsadi, mphatso zabwino. (KUKONZEKERA KOLASI) Panopa tikudikirabe (KOLASI) Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka. Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu. M’dziko labwino. 2. Mwayi wathu timangeko nyumba M’lungu watidalitsa. Njala yatha, chakudya paliponse ngakhaletu m’mapiri. Kulira titaiwala, zosangalatsa! Mavuto onse atatha, atatha, atha! (KOLASI) Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka. Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu. M’dziko labwino. (VESI LOKOMETSERA) Panopa chiyembekezo chathuchi chikule. Pompano Tilowa m’dziko labwino Lokoma. (KOLASI) Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka. Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu. (KOLASI) Tidzatukuladi mitu yathu ndi kupulumuka. Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu. M’dziko labwino. (MAWU OMALIZA) Pompano—pompano Zitheka. Pompano—pompano Tilowa. Pompano—pompano Zitheka. Pompano—pompano Tilowa. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena “M’dziko Labwino” NYIMBO ZATHU “M’dziko Labwino” Chinenero Chamanja cha ku Malawi “M’dziko Labwino” https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014392/univ/art/1014392_univ_sqr_xl.jpg