NTCHITO YOLALIKIRA YAPADERA

Kuphunzira Baibulo Mwaulere

Yeserani kuphunzira Baibulo mochita kukambirana pogwiritsa ntchito kabuku katsopano kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale.

 

Dziwani Zambiri

Onerani Baibulo pa Intaneti

Onani zimene zili mu Baibulo la Dziko Latsopano lomwe ndi lolondola komanso losavuta kuwerenga.

Onerani Baibulo pa Intaneti

Onani zimene zili mu Baibulo la Dziko Latsopano lomwe ndi lolondola komanso losavuta kuwerenga.

Onani mavidiyo, nyimbo ndi nkhani zimene zangoikidwa kumene.

Onani Zatsopano

Yambani kuphunzira Baibulo

Phunzirani Baibulo kwaulere, mochita kukambirana ndi mphunzitsi wanu.

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova.

Fikani Pamsonkhano

Dziwani zambiri zokhudza misonkhano yathu. Pezani malo apafupi amene kumachitikira misonkhano yathu.

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa?

Ndife anthu ochokera m’mitundu, zikhalidwe ndiponso zinenero zosiyanasiyana, koma ndife ogwirizana kwambiri chifukwa cholinga chathu n’chimodzi. Cholinga chathu chachikulu n’kulemekeza Yehova, Mulungu wotchulidwa m’Baibulo ndiponso Mlengi wa zinthu zonse. Timayesetsa kutsanzira Yesu Khristu ndipo timanyadira kutchedwa Akhristu. Nthawi zonse aliyense wa ife amathera nthawi yake pothandiza ena kuphunzira Baibulo ndiponso za Ufumu wa Mulungu. Timatchedwa kuti Mboni za Yehova chifukwa choti timachitira umboni, kapena kuti kulalikira za Yehova Mulungu ndi Ufumu wake.

Fufuzani pa Webusaiti yathuyi. Werengani Baibulo pa Intaneti. Dziwani zambiri za ifeyo ndiponso zimene timakhulupirira.

 

Anthu Awiri a Mboni za Yehova Akulalikira Munthu Wina Mmunda wa Mphunga.