Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Zili M’magaziniyi

Zimene Zili M’magaziniyi

M’dzikoli muli mavuto. Nthawi iliyonse tikhoza kukumana ndi ngozi zam’chilengedwe komanso mavuto oyambitsidwa ndi anthu. Kodi inuyo kapena anthu a m’banja lanu mungapirire bwanji mavuto amene mukukumana nawo? Dziwani zimene mungachite kuti:

1 | Muziteteza Thanzi Lanu

2 | Muzisamala Ndalama

3 | Muziteteza Ubwenzi Wanu ndi Anzanu

4 | Muziteteza Chiyembekezo Chanu