Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

M’kope Ino ya Galamuka!

M’kope Ino ya Galamuka!

M’dziko la mavutoli, nthawi iliyonse aliyense wa ife angakumane na mavuto monga matsoka a zacilengedwe kapena mavuto ena ocititsidwa na anthu. Kodi inu na banja lanu mungadziteteze bwanji ku mavuto amenewa? Phunzilani mmene:

1 | Mungatetezele Thanzi Lanu

2 | Mungatetezele Cuma Canu

3 | Mungatetezele Ubale Wanu na Ena

4 | Mungalimbitsile Ciyembekezo Canu