Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Chikuto cha Kumapeto

Chikuto cha Kumapeto

Ponena za Yehova Mulungu, lemba la Yesaya 40:11 limati: “Iye adzasamalira gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa. Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa, ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.” Mukaona m’busa atanyamula kamwana ka nkhosa pachifuwa pake, kodi nanunso mumafunitsitsa mutayandikira Atate wanu wakumwamba choncho? Koma kodi mungatani kuti muyandikire Yehova?