Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mtima Wanu

Mtima Wanu

Chigawo 7

Mtima Wanu

Kodi mumaona kuti ndinu munthu wotani?

□ Wosachedwa kupsa mtima.

□ Wolephera ndiponso womangolakwitsa chilichonse.

□ Wongokhalira kudandaula.

□ Wongokhalira kuganiza za atsikana kapena anyamata.

□ Wofuna kugonana ndi atsikana kapena anyamata anzanga.

Ngati mwachonga chilichonse pa zinthu zimenezi, musataye mtima, chifukwa Mitu 26 mpaka 29 ikuthandizani pankhani zimenezi.

[Chithunzi chachikulu pamasamba 216, 217]