Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Nyimbo 36

“Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”

“Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”

(Mateyo 19:5, 6)

1. Mulungu ndi anthu

Amva malonjezo.

Chingwe cholimba bwino

Chamangidwa lero.

Awa alonjezana

Kuti akondane.

(KOLASI)

‘Chomwe M’lungu wamanga

Musalekanitse.’

2. Cholinga cha M’lungu

Anachifufuza.

Kupeza madalitso

N’komwe akufuna.

Awa agwirizana

Kuti akondane.

(KOLASI)

‘Chomwe M’lungu wamanga

Musalekanitse.’

(Onaninso Gen. 2:24; Mla. 4:12; Aef. 5:22-33.)