Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Nyimbo 79

Kukoma Mtima Ndi Khalidwe Lofunika Kwambiri

Kukoma Mtima Ndi Khalidwe Lofunika Kwambiri

(Aefeso 4:32)

1. Tikuthokoza chifukwa choti

Yehova tam’dziwa.

Ngakhale n’ngwanzeru ndi wamphamvu,

Iye ndi wokoma mtima.

2. Yesu akuitana otopa

Awatsitsimule.

Ndipo goli lake ndi lofewa

Chifukwa n’ngokoma mtima.

3. Mulungu komanso Mbuye Yesu

Tiziwatsanzira.

M’zochita zathu tifunikira

Kukhala okoma mtima.

(Onaninso Mika 6:8; Mat. 11:28-30; Akol. 3:12; 1 Pet. 2:3.)