CHIGAWO 10 Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? YAMBANI Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Ambiri mwa anthu amene anamwalira adzaukitsidwa padziko lapansi. Machitidwe 24:15 Pali madalitso ambiri amene mudzalandire m’tsogolo muno ngati mukumvera Yehova. Mudzakhala ndi thanzi labwino ndipo palibe amene adzadwale, kulumala kapena kukalamba. Mudzatha kukhulupirira munthu aliyense chifukwa sikudzakhala anthu oipa. Sikudzakhala zinthu zilizonse zopweteka, chisoni kapenanso kulira. Palibe amene adzakalambe ndi kufa. Mudzasangalala kukhala pamodzi ndi anzanu komanso achibale anu ndipo moyo udzakhala wosangalatsa kwambiri m’Paradaiso. Anthu adzakhala mopanda mantha ndipo adzakhaladi osangalala. Ufumu wa Mulungu udzathetsa mavuto onse. Chivumbulutso 21:3, 4 Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Ali padziko lapansi, Yesu anafotokoza kwambiri za Ufumu wa Mulungu kuposa nkhani ina iliyonse. Kwa zaka zambiri otsatira ake akhala akupempherera Ufumu umenewu kuti ubwere. NTCHITO YOLALIKIRA YAPADERA N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo—Vidiyo Yathunthu Baibulo likuthandiza anthu ambirimbiri padziko lonse lapansi kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mungakonde? MABUKU Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zifukwa ziwiri zotichititsa kukhulupirira zimene Baibulo limanena zokhudza tsogolo labwino. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? MVERANI MULUNGU KUTI MUDZAPEZE MOYO WOSATHA Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/e781f8601f/images/syn_placeholder_sqr.png