Mawu Oyamba YAMBANI Mawu Oyamba Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Mulungu ali ngati bambo amene amakonda kwambiri ana ake. 1 Petulo 5:6, 7 Mulungu ndi Mlengi wathu, ndipo amatisamalira mwachikondi. Mofanana ndi bambo wanzeru komanso wachikondi amene amalangiza ana ake, Mulungu amaphunzitsa anthu ake padziko lonse zoyenera kuchita kuti akhale ndi moyo wabwino. Mulungu amatiphunzitsa choonadi chamtengo wapatali chimene chimatisangalatsa ndiponso kutipatsa chiyembekezo. Mukamamvera Mulungu, adzakutsogolerani ndi kukutetezani, ndiponso adzakuthandizani kuti muthane ndi mavuto amene mukukumana nawo. Kuwonjezera pamenepo, mudzakhala ndi moyo wosatha. Mulungu akutiuza kuti: “Bwerani kwa ine. Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.” Yesaya 55:3 Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS Kodi Mulungu Ali Ndi Dzina? Mulungu ali ndi maina ambiri audindo monga akuti Atate, Mlengi ndi Ambuye. Koma Dzina lake lenileni limapezeka m’Baibulo malo oposa 7000. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mawu Oyamba MVERANI MULUNGU KUTI MUDZAPEZE MOYO WOSATHA Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha—Mawu Oyamba Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha—Mawu Oyamba https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/e781f8601f/images/syn_placeholder_sqr.png